2 Mbiri 22:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakulanga Yehu nyumba ya Ahabu, anapeza akalonga a Israyeli, ndi ana a abale a Ahaziya, akutumikira Ahaziya, nawapha.

2 Mbiri 22

2 Mbiri 22:4-12