2 Mbiri 22:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuonongeka kwa Ahaziya tsono nkwa Mulungu, kuti amuke kwa Yehocamu; pakuti atafika anaturukira pamodzi ndi Yehoramu kukayambana ndi Yehu mwana wa Nimsi, amene Yehova anamdzoza alikhe nyumba ya Ahabu.

2 Mbiri 22

2 Mbiri 22:1-9