2 Mbiri 22:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anayendanso m'kupangira kwao, namuka pamodzi ndi Yehoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Israyeli, kukayambana nkhondo ndi Hazaeli mfumu ya Aramu ku Ramoti Gileadi; ndipo Aaramu anamlasa Yehoramu.

2 Mbiri 22

2 Mbiri 22:1-12