2 Mbiri 22:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacita coipa pamaso pa Yehova, monga umo anacitira a nyumba ya Ahabu; pakuti ompangira ndi iwowa, atamwalira atate wace; ndi kuonongeka kwace nkumeneko.

2 Mbiri 22

2 Mbiri 22:1-7