2 Mbiri 21:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anali wa zaka makumi atatu mphambu ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka zisanu ndi zitatu, namuka wopanda wina womlakalaka; ndipo anamuika m'mudzi wa Davide, koma si m'manda a mafumu ai.

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:17-20