2 Mbiri 21:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, itapita nthawi, pakutha pace pa zaka ziwiri, anaturuka matumbo ace mwa nthenda yace namwalira nazo nthenda zoipa, Ndipo anthu ace sanampserezera zonunkhira, monga umo anapserezera makolo ace.

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:18-20