2 Mbiri 21:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma mwayenda m'njira ya mafumu a Israyeli, ndi kucititsa Yuda ndi okhala m'Yerusalemu cigololo, monga umo anacitira cigololo a nyumba ya Ahabu, mwaphanso abale anu a nyumba ya atate wanu, ndiwo abwino akuposa inu;

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:11-14