2 Mbiri 21:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamdzera kalata wofuma kwa Eliya mneneri, ndi kuti, Atero Yehova Mulungu wa Davide atate wanu, Popeza simunayenda m'njira za Yehosafati atate wanu, kapena m'njira za Asa mfumu ya Yuda,

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:4-18