2 Mbiri 20:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi tsiku lacinai anasonkhana m'cigwa ca Beraka; pakuti pamenepo analemekeza Yehova; cifukwa cace anacha dzina lace la malowo, Cigwa ca Beraka, mpaka lero lino.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:25-31