2 Mbiri 20:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pofika Yehosafati ndi anthu ace kutenga zofunkha zao, anapezako cuma cambiri, ndi mitembo yambiri, ndi zipangizo zofunika, nadzifunkhira, osakhoza kuzisenza zonse; nalimkutenga zofunkhazo masiku atatu, popeza zinacuruka.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:22-32