2 Mbiri 20:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nati iye, Tamverani Ayuda inu nonse, ndi inu okhala m'Yerusalemu, ndi inu mfumu Yehosafati, atero nanu Yehova, Musaope musatenge nkhawa cifukwa ca aunyinji ambiri awa; pakuti nkhondoyi si yanu, koma ya Mulungu.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:14-20