2 Mbiri 20:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mzimu wa Yehova unagwera Yahazieli mwana wa Zekriya, mwana wa Benaya, mwana wa Yetieli, mwana wa Mataniya, Mlevi, wa ana a Asafu, pakati pa msonkhano;

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:4-23