2 Mbiri 18:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mfumu ya Israyeli tsono ndi Yehosafati mfumu ya Yuda anakhala yense pa mpando wacifumu wace, obvala zobvala zacifumu zao, nakhala pamalo poyera polowera pa cipata ca Samariya; ndi aneneri onse ananenera pamaso pao.

2 Mbiri 18

2 Mbiri 18:4-18