2 Mbiri 18:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Zedekiya mwana wa Kenana anadzisulira nyanga zacitsulo, nati, Atero Yehova, Ndi izi udzagunda Aaramu mpaka adatha psiti.

2 Mbiri 18

2 Mbiri 18:8-12