2 Mbiri 18:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Ahabu mfumu ya Israyeli kwa Yehosafati mfumu ya Yuda, Mupita nane kodi ku Ramoti Gileadi? Nayankha, nati, Monga inu momwemo ine; monga anthu anu momwemo anthu anga; tidzakhala nanu ku nkhondoyi.

2 Mbiri 18

2 Mbiri 18:2-8