2 Mbiri 18:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zitatha zaka zina, anatsikira kwa Ahabu ku Samariya. Ndi Ahabu anamphera iye ndi anthu anali naye nkhosa, ndi ng'ombe zocuruka; namnyenga akwere naye pamodzi ku Ramoti Gileadi.

2 Mbiri 18

2 Mbiri 18:1-4