2 Mbiri 11:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rehabiamu anadzitengera mkazi Mahalati, mwana wamkazi wa Yerimoti mwana wa Davide, ndi wa Abihaili mwana wamkazi wa Eliabu mwana wa Jese;

2 Mbiri 11

2 Mbiri 11:9-22