2 Mbiri 11:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo analimbikitsa ufumu wa Yuda, nalimbikitsa Rehabiamu, mwana wa Solomo zaka zitatu; pakuti anayenda m'njira ya Davide ndi Solomo zaka zitatu.

2 Mbiri 11

2 Mbiri 11:9-23