2 Mbiri 1:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nakwerako Solomo ku guwa la nsembe pamaso pa Yehova linali ku cihema cokomanako, napereka pamenepo nsembe zopsereza cikwi cimodzi.

2 Mbiri 1

2 Mbiri 1:4-15