2 Mbiri 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Guwa la nsembe lomwe lamkuwa, adalipanga Bezaleli mwana wa Uri mwana wa Huri linali komweko, ku khomo la kacisi wa Yehova; ndipo Solomo ndi khamulo anafunako.

2 Mbiri 1

2 Mbiri 1:3-7