2 Mbiri 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo ndi khamu lonse pamodzi naye anamuka ku msanje wa ku Gibeoni; pakuti kumeneko kunali cihema cokomanako ca Mulungu adacimanga Mose mtumiki wa Yehova m'cipululu.

2 Mbiri 1

2 Mbiri 1:2-4