2 Mbiri 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo analankhula ndi Aisrayeli onse, ndi akuru a zikwi ndi a mazana, ndi kwa oweruza, ndi kwa kalonga ali yense wa Israyeli, akuru a nyumba za makolo.

2 Mbiri 1

2 Mbiri 1:1-7