2 Mbiri 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Solomo anadza ku Yerusalemu kucokera ku msanje uli ku Gibeoni, ku khomo la cihema cokomanako; ndipo anacita ufumu pa Israyeli.

2 Mbiri 1

2 Mbiri 1:5-16