2 Mafumu 9:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pociona ici Ahaziya mfumu ya Yuda anathawa njira ya ku khumbi la m'munda. Namtsata Yehu, nati, Mumkanthe uyonso pagareta; namkantha pa cikweza ca Guru ciri pafupi pa Yibleamu. Nathawira iye ku Megido, namwalira komweko.

2 Mafumu 9

2 Mafumu 9:24-30