2 Mafumu 8:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo caka cacisanu ca Yoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Israyeli, pokhala Yehosafati mfumu ya Yuda, Yehoramu mwana wa Yehosafati analowa ufumu.

2 Mafumu 8

2 Mafumu 8:12-26