2 Mafumu 8:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali m'mawa mwace, anatenga cimbwi, nacibviika m'madzi, naciphimba pankhope pa mfumu, nifa; ndipo Hazaeli analowa ufumu m'malo mwace.

2 Mafumu 8

2 Mafumu 8:8-21