2 Mafumu 7:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naturuka anthu, nafunkha m'misasa ya Aaramu. Ndipo anagula miyeso wa ufa ndi sekeli, nagulanso miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, monga umo adanenera Yehova.

2 Mafumu 7

2 Mafumu 7:9-18