2 Mafumu 6:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mtima wa mfumu ya Aramu unabvutika kwambiri pa icico, naitana anyamata ace, nanena nao, Kodi simudzandiuza wina wa ife wobvomerezana ndi mfumu ya Israyeli ndani?

2 Mafumu 6

2 Mafumu 6:9-18