2 Mafumu 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu ya Israyeli inatumiza kumene munthu wa Mulungu anamuuzako ndi kumcenjeza; nadzisunga osapitako, kawiri kawiri.

2 Mafumu 6

2 Mafumu 6:9-19