2 Mafumu 4:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naturuka wina kukachera ndiwo kuthengo, napeza conga ngati mpesa, nacherapo zipuzi kudzaza m'pfunga mwace, nadza, nazicekera-cekera m'nkhali ya cakudya, popeza sanazidziwa.

2 Mafumu 4

2 Mafumu 4:36-44