2 Mafumu 3:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anafika ku misasa ya Israyeli, Aisrayeli ananyamuka, nakantha Amoabu, nathawa iwo pamaso pao; ndipo analowa m'dziko ndi kukantha Amoabu.

2 Mafumu 3

2 Mafumu 3:22-26