2 Mafumu 25:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali caka cacisanu ndi cinai ca ufumu wace, mwezi wakhumi, tsiku lakhumi la mwezi, Nebukadinezara mfumu ya Babulo, iye ndi khamu lace lonse anadzera Yerusalemu, naumangira misasa, naumangira timalinga mouzinga.

2 Mafumu 25

2 Mafumu 25:1-7