2 Mafumu 22:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Safani mlembiyo anadza kwa mfumu, nambwezera mfumu mau, nati, Anyamata anu anakhuthula ndalama zopereka m'nyumba, nazipereka m'dzanja la anchito akuyang'anira nyumba ya Yehova.

2 Mafumu 22

2 Mafumu 22:5-19