2 Mafumu 22:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hilikiya mkulu wa ansembe anati kwa Safani mlembi, Ndapeza buku la cilamulo m'nyumba ya Yehova. Napereka Hilikiya bukulo kwa Safani, iye naliwerenga.

2 Mafumu 22

2 Mafumu 22:1-16