2 Mafumu 21:25-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Macitidwe ena tsono a Amoni adawacita, salembedwa kodi m'buku la macitidwe a mafumu a Yuda?

26. Naikidwa iye m'manda mwace m'munda wa Uza; nakhalamfumum'malo mwace Yosiya mwana wace.

2 Mafumu 21