2 Mafumu 2:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anamuumiriza kufikira anacita manyazi; pamenepo anati, Tumizani. Motero anatumiza amuna makumi asanu, namfunafuna iwo masiku atatu, osampeza.

2 Mafumu 2

2 Mafumu 2:16-25