2 Mafumu 2:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena naye, Taonani, tsono anyamata anufe tiri nao amuna makumi asanu amphamvu, amuke kukafuna mbuye wanu; kapena wamkweza mzimu wa Yehova ndi kumponya pa phiri lina, kapena m'cigwa dna. Koma anati, Musatumiza.

2 Mafumu 2

2 Mafumu 2:13-23