2 Mafumu 19:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamva za Tirihaka mfumu ya Kusi, akuti, Taonani, waturuka kuthirana nawe nkhondo. Pamenepo anatumizanso mithenga kwa Hezekiya, ndi kuti,

2 Mafumu 19

2 Mafumu 19:1-14