2 Mafumu 19:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muzitero naye Hezekiya mfumu ya Yuda, kuti, Asakunyenge Mulungu wako amene umkhulupirira, ndi kuti, Yerusalemu sudzaperekedwa m'dzanja la mfumu ya Asuri.

2 Mafumu 19

2 Mafumu 19:6-15