2 Mafumu 18:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anakhulupirira Yehova Mulungu wa Israyeli; atafa iye panalibe wakunga iye mwa mafumu onse a Yuda, ngakhale mwa iwo okhalapo asanabadwe iye.

2 Mafumu 18

2 Mafumu 18:1-8