2 Mafumu 16:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nalicotsa guwa la nsembe lamkuwa linali pamasopa Yehova, nalicotsa kukhomo la nyumba pakati pa guwa la nsembe lace ndi nyumba ya Yehova, naliikakumpotokwa guwa la nsembe lace.

2 Mafumu 16

2 Mafumu 16:5-20