2 Mafumu 16:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nafukiza nsembe yace yopsereza ndi nsemba yace yaufa, natsanulira nsembe yace yothira, nawaza mwazi wa nsembe zace zamtendere pa guwa la nsembelo,

2 Mafumu 16

2 Mafumu 16:5-20