2 Mafumu 15:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiye wa zaka makumi awiri mphambu: zisanu polowa ufumu wace, nakhalamfumu zaka khumi ndi zisanu ndi cimodzi m'Yerusalemu; ndipo dzina la mace ndiye Yerusa mwana wa Zadoki.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:29-37