2 Mafumu 15:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka caciwiri ca Peka mwana wa Remaliya mfumu ya Israyeli, Yotamu mwana wa Uziya mfumu ya Yuda analowa ufumu wace.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:22-33