2 Mafumu 15:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Salumu mwana wa Yabesi anamcitira ciwembu, namkantha pamaso pa anthu, namupha; nakhala mfumu m'malo mwace.

2 Mafumu 15

2 Mafumu 15:4-11