2 Mafumu 14:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Macitidwe ena tsono a Yerobiamu, ndi zonse anazicita, ndi mphamvu yace, umo anacita nkhondo, nabweza kwa Israyeli Damasiko ndi Hamati amene anali a Yuda, sizilembedwa kodi m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli?

2 Mafumu 14

2 Mafumu 14:19-29