2 Mafumu 14:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova sadanena kuti adzafafaniza dzina la Israyeli pansi pa thambo; koma anawapulumutsa ndi dzanja la Yerobiamu mwana wa Yoasi.

2 Mafumu 14

2 Mafumu 14:18-29