2 Mafumu 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu sanalekana nazo zolakwa za nyumba ya Yerobiamu, zimene analakwitsa nazo Israyeli, nayenda m'mwemo; nicitsalanso cifanizo m'Samariya.

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:2-14