2 Mafumu 13:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anapatsa Israyeli mpulumutsi, naturuka iwo pansi pa dzanja la Aaramu; nakhala ana a Israyeli m'mahema mwao monga kale.

2 Mafumu 13

2 Mafumu 13:3-10