2 Mafumu 11:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

napenya, ndipo taonani, mfumu iri ciriri paciundo, monga adafocita, ndi atsogoleri ndi amalipenga pali mfomu; nakondwerera anthu onse a m'dziko, naomba malipenga. Pamenepo Ataliya anang'amba zobvala zace, napfuula, Ciwembu, Ciwembu.

2 Mafumu 11

2 Mafumu 11:4-20